YODALITSIKA NDIYO MBUTO (#13493)

Yodalitsika ndiyo mbuto, ndi nyumba, ndi malo, ndi mzinda, ndi mtima, ndi phiri, ndi pothawira, ndi phanga, ndi chigwa, ndi mtunda, ndi nyanja, ndi chilumba, ndi dambo, kumene dzina la Mulungu latchulidwako, ndi chitamando Chake chalemekedwako.

-Bahá'u'lláh
-----------------------

